Ngati alimi adzapatsidwa mwayi wogulitsa ku malo abwino, mpombe ungakhale gwero la chuma kwa iwo komanso kwa dera lonse la Balaka. Pakadali pano, alimi akupempha boma kuti liwathandize kupeza misika ...